Hadith #405Hadith #405

Hadith #405

Chichewa (Chicheŵa)

Zinthu zisanu ndi zachilengedwe nthupi mwanu : Kuvinidwa, kumeta tsitsi malo obisika, kupungula ndevu za pa mwamba pa mlomo, kuwenga zikhadabo, komanso ndikumeta tsitsi laku nkhwapa.

Reference: صحیح مسلم، كتاب الطهارة، باب خصال الفطرة، الحدیث 257

Available in Other Languages