
Hadith #343
Chichewa (Chicheŵa)Yemwe angadzuke mwainu ku m'mawa ali ndi mtendele wamu mtima, wathanzi nthupi mwake, komanso ali ndi chakudya cha tsiku limenelo zili ngati dziko lonse lapansi lasonkhanitsidwa kwa iye.
Reference: جامع الترمذي، أبواب الزهد، باب في توكل على الله، الحدیث 2346