
Hadith #178
Chichewa (Chicheŵa)Wozenga milandu akapereka chigamulo ndikuyesetsa njira zonse kuti alondole, ndikulondoladi (muchigamulo chake), amapeza malipiro awiri, ndipo ngati walakwitsa, amakhala ndi malipiro amodzi.
Reference: صحيح البخاري، كتاب الاعتصام بالكتاب والسنة، باب أجر الحاكم إذا اجتهد فأصاب أو أخطأ، الحدیث 7352