Hadith #357Hadith #357

Hadith #357

Chichewa (Chicheŵa)

Uopeni umbombo chifukwa umbombo unaonongesa mibado yomwe inalipo inu musanabwere, mpakana anaphana komanso anaziloleza zinthu zomwe zinali zoletsedwa kwa iwo.

Reference: صحيح مسلم، كتاب البر والصلة والآداب، باب تحريم الظلم، الحديث 2578

Available in Other Languages