Hadith #92Hadith #92

Hadith #92

Chichewa (Chicheŵa)

Silimukhudza Msilamu vuto lina lililonse monga, kutopa, matenda, nkhawa, madandaulo, kupweteka komanso zowawa, ngakhale kubaidwa ndi minga, kupatula kuti (kudzera mu mavutowa) Allah amamuchotsera machimo ake.

Reference: صحيح البخاري، كتاب المرضى، باب ما جاء في كفارة المرض، الحدیث 5641

Available in Other Languages