
Hadith #180
Chichewa (Chicheŵa)Pilirani, chifukwa sikubwera nthawi ina iliyonse kupatula kuti nthawi yapambuyo pake ndiyoipa kuposa iyo, kufikira pamene mudzakumane ndi Mbuye wanu.
Reference: صحيح البخاري، كتاب الفتن، باب لا يأتي زمان إلا الذي بعده شر منه، الحدیث 7068