
Hadith #118
Chichewa (Chicheŵa)Paradizo ili pafupi ndi wina aliyense wa inu kuposa kuwandikira kwa chingwe cha nsapato yake, izi ndichimodzimodzi ndi kuwandikira kwa moto wa gahena.
Reference: صحيح البخاري، كتاب الرقاق، باب الجنة أقرب إلى أحدكم۔۔۔الخ، الحدیث 6488