
Hadith #253
Chichewa (Chicheŵa)Ngati mavuto ena aliwonse akupeza, usanene kuti ndikanapanga chakuti, zikanakhala mwakuti. koma nena kuti ichi ndichikonzero cha Allah. Ndipo Iye amachita chimene wafuna. Liwu loti, "nkanatere" ndichiyambi cha ntchito za satana.
Reference: صحيح مسلم، كتاب القدر، باب في الأمر بالقوة وترك العجز، الحدیث 2664