Hadith #300Hadith #300

Hadith #300

Chichewa (Chicheŵa)

Ngati kutatentha kwambiri, dikilirani ndikupemphera Dhuhur kutazizilirako, chifukwa kuchuluka kwa kutentha kumachokera mumpweya waku jahena.

Reference: صحیح البخاري، ‌‌باب: الإبراد بالظهر في شدة الحر، الحدیث 536

Available in Other Languages