
Hadith #85
Chichewa (Chicheŵa)Ndizosaloledwa kwa msilamu kukwiyira m'bale wake kwa masiku opambana atatu, munthu amene angamkwiyire m'bale wake kupitilira masiku atatu, kenako ndikumwalira ali choncho, adzalowa ku moto.
Reference: سنن أبي داود، كتاب الأدب، باب فيمن يهجر أخاه المسلم، الحدیث 4914