
Hadith #350
Chichewa (Chicheŵa)Ndithudi usiku muli nthawi imene, msilamu sangampemphe Mulungu mu zofuna zake za dziko lapansi ndi akhera kupatula kuti Mulungu adzampatsa, ndipo zimenezi zimachitika usiku uliwonse.
Reference: صحيح مسلم، كتاب صلاة المسافرين وقصرها، باب أفضل الصلاة طول القنوت، الحدیث 757