
Hadith #400
Chichewa (Chicheŵa)Ndithudi fanizo la munthu oloweza Qur'an lili ngati fanizo la Ngamila yomwe yamangidwa ndi chingwe chake ku chintengo(ndi mwini wake) mulimonse angapitire akaipeza, koma ngati angaisiye osaimangilira idzapita.
Reference: صحيح مسلم، كتاب صلاة المسافرين وقصرها، باب الأمر بتعهد القرآن...إلخ، الحدیث 789