
Hadith #245
Chichewa (Chicheŵa)Ndithu manda ndi nyumba yoyamba munyumba za dziko lili nkudza, amene angapulumukemo, umoyo wapambuyo pake udzakhala wosavuta, koma ngati sangapulumuke (m'mandamo), komwe kukubwerako ndikopweteka kwambiri kuposa m'mandamo.
Reference: سنن ابن ماجه، كتاب الزهد، باب ذكر القبر والبلى، الحدیث 4267