
Hadith #251
Chichewa (Chicheŵa)Ndithu ku Jannah kuli masitepe okwanira zana limodzi (100) omwe Allah wawakonzera anthu omenya nkhondo munjira yake. Pakati pa masitepe awiri aliwonse pali mtunda wofanana ndiwapakati pa nthaka ndikumwamba.
Reference: صحيح البخاري، كتاب الجهاد والسير، باب درجات المجاهدين في سبيل الله، الحدیث 2790