Hadith #297Hadith #297

Hadith #297

Chichewa (Chicheŵa)

Ndithu Angelo amakhala akumpemphera chikhululuko munthu amene wasala kudya ngati chakudya chitadyedwa (ndi anthu ena) pamaso pake, kufikira anthuwo atamaliza.

Reference: جامع الترمذي، أبواب الصوم، ‌‌باب ما جاء في فضل الصائم إذا أكل عنده، الحدیث 785

Available in Other Languages