Hadith #206Hadith #206

Hadith #206

Chichewa (Chicheŵa)

Ndithu Allah anakhululukira anthu anga chifukwa cha ine muzolakwika, muzoiwala , komanso pa zinthu zomwe angachite mosafuna (mokakamizidwa).

Reference: سنن ابن ماجه، كتاب الطلاق، باب طلاق المكره والناسي، الحدیث 2043

Available in Other Languages