
Hadith #226
Chichewa (Chicheŵa)Ndili ndi maina asanu (5): Ine ndi Muhammad, Ahmad, Al-Mahi (amene Allah adzathetsa kusakhulupirira kudzera mwa iye), inenso ndi Al-Haashir (amene anthu adzasonkhane kwa iye) komanso ndine Al-Aaqib (womaliza amene pambuyo pake palibe Mtumiki).
Reference: صحيح البخاري، كتاب المناقب، باب ما جاء في أسماء رسول الله ﷺ، الحدیث 3532