Hadith #202
Chichewa (Chicheŵa)Ndili ndi chiyembekezo mwa Allah kuti kusala kwa tsiku la Arafah kumafufuta machimo a chaka cham'mbuyo komanso a chaka chotsatira.
Reference: صحيح مسلم، كتاب الصيام، باب استحباب صيام ثلاثة أيام۔۔۔إلخ، الحدیث 1162

Ndili ndi chiyembekezo mwa Allah kuti kusala kwa tsiku la Arafah kumafufuta machimo a chaka cham'mbuyo komanso a chaka chotsatira.
Reference: صحيح مسلم، كتاب الصيام، باب استحباب صيام ثلاثة أيام۔۔۔إلخ، الحدیث 1162