Hadith #291Hadith #291

Hadith #291

Chichewa (Chicheŵa)

Musamutukwane tambala akamakuwa, chifukwa iye amadzutsa anthu kuti akapemphere.

Reference: سنن أبي داود، ‌‌‌‌أبواب النوم، باب ما جاء في الديك والبهائم، الحدیث 5101

Available in Other Languages