
Hadith #166
Chichewa (Chicheŵa)Munthu wosala kudya ali ndizisangalalo ziwiri: chisangalalo panthawi yomasula komanso chisangalalo pamene adzakumane ndi Mbuye wake (Allah).
Reference: صحيح البخاري، كتاب التوحيد، باب قول الله تعالى: يريدون أن يبدلوا كلام الله، الحدیث 7492