
Hadith #95
Chichewa (Chicheŵa)Munthu wolumikiza ubale si amene amakhala akubwenzera zabwino, koma wolumikiza ubale weni weni ndi amene amaulumikiza pamene abale ake akuuthetsa ubalewo.
Reference: صحيح البخاري، كتاب الأدب، باب ليس الواصل بالمكافئ، الحدیث 5991