
Hadith #94
Chichewa (Chicheŵa)Munthu wokhulupilira amene amakhala ndi anthu ndikumapilira ku zoipa (zokhumudwitsa) zawo, ndiwabwino kwambiri kuposa munthu amene samakhala limodzi ndi anthu komanso samapilira ku zoipa (zokhumudwitsa) zawo.
Reference: الأدب المفرد للبخاري، باب الذي يصبر على أذى الناس، الحدیث 388