Hadith #396Hadith #396

Hadith #396

Chichewa (Chicheŵa)

Munthu amene angaphunzire maphunziro omwe umapeza nawo chisangalalo cha Allah, sakuwaphunzira koma ndi cholinga chopeza za dziko lapansi, sakalimva fungo kaku Janna.

Reference: سنن أبي داود، کتاب العلم، باب في طلب العلم لغير الله تعالى، الحدیث 3664‌‌

Available in Other Languages