Hadith #402Hadith #402

Hadith #402

Chichewa (Chicheŵa)

Munthu amene angaphe buluzi ndi mwala umodzi ali ndi malipiro 100, ngati angaphe ndi mwala wachiwiri ndie kuti ali ndi malipiro ocheperako, ngatinso angaphe ndi wa chitatu alinso ndi malipiro apansi pake.

Reference: صحیح مسلم، كتاب البر والصلة والآداب، باب النهي عن لعن الدواب وغيرها، الحدیث 2240

Available in Other Languages