
Hadith #82
Chichewa (Chicheŵa)Munthu amene angakonde mzake chifukwa cha Allah, angadane ndi wina wake chifukwa cha Allah, amene amapereka chifukwa cha Allah komanso amaletsa chifukwa cha Allah, ameneyo wakwaniritsa chikhulupiliro chake.
Reference: سنن أبي داود، كتاب السنة، باب الدليل على زيادة الإيمان ونقصانه، الحدیث 4681