Hadith #160Hadith #160

Hadith #160

Chichewa (Chicheŵa)

Munthu amene angaiwale kuti wasala ndikudya kapena kumwa, ayenera kupitiriza kusala kwake chifukwa Allah ndi amene wamudyetsa ndikumumwetsa.

Reference: صحيح مسلم، كتاب الصيام، باب أكل الناسي وشربه وجماعه لايفطر، الحدیث 1155

Available in Other Languages