
Hadith #15
Chichewa (Chicheŵa)Munthu amene angagwiritsitse sunnah yanga mu nthawi ya chiwonongeko kwa anthu anga, iyeyo amapeza malipiro ama shaheed(omwalirira mu njira ya Allah) okwana zana limodzi (100)
Reference: (مشكاۃ المصابيح، كتاب الإیمان، باب الاعتصام، الحدیث 176)