Hadith #190Hadith #190

Hadith #190

Chichewa (Chicheŵa)

Munthu akadwala kapena akakhala paulendo, amakhala akulembedwera malipiro ofanana ndi zimene ankachita pamene anali wangwiro komanso asali paulendo.

Reference: صحيح البخاري، كتاب الجهاد والسير، ‌‌باب يكتب للمسافر مثل ما كان يعمل في الإقامة، الحدیث 2996

Available in Other Languages