
Hadith #391
Chichewa (Chicheŵa)Mulungu akamfunira zabwino kapolo wake amampatsiratu zilangu pa dziko lapansi pompano, ndipo akamfunira zoipa amamuchedwetsera chilangacho kuti akamulange ndi uchimo wakewo tsiku lomaliza.
Reference: جامع الترمذي، أبواب الزهد، باب ما جاء في الصبر على البلاء، الحدیث 2396