
Hadith #321
Chichewa (Chicheŵa)M'modzi wa inu akafuna kudya, ayenera kudyera dzanja lamanja, ndipo akafuna kumwa, ayenera kumwera dzanja lamanja chifukwa satana amadyera ndikumwera dzanja lamanzere.
Reference: صحيح مسلم، كتاب الأشربة، باب آداب الطعام والشراب وأحكامهما، الحدیث 2020