
Hadith #91
Chichewa (Chicheŵa)Maso awiri sadzakhudzidwa ndi moto (wa gahena): Diso limene limalira chifukwa choopa Allah. Komanso diso limene siligona kukhala tcheru munjira ya Allah.
Reference: جامع الترمذي، أبواب فضائل الجهاد، باب ما جاء في فضل الحرس في سبيل الله، الحدیث 1639