Hadith #174Hadith #174

Hadith #174

Chichewa (Chicheŵa)

Mapemphero asanu atsiku ndi tsiku, kuchokera pemphero la Jumuah kukafika Jumuah ina komanso kuchokera Ramadan kukafika Ramadan ina, zinthu zimenezi zimafufuta machimo amene apangidwa pakati pawo ngati munthuyo wazitalikitsa kumachimo akulu-akulu.

Reference: صحيح مسلم، کتاب الطهارة، باب الصلاة الخمس۔۔۔الخ، الحدیث 233

Available in Other Languages