Hadith #397Hadith #397

Hadith #397

Chichewa (Chicheŵa)

Magulu atatu awanthu sakawayankhulitsa Mulungu tsiku lomaliza, sakawayeretsa kuzolakwa zawo, sakawayang'ana mwachisoni ndipo adzakhala ndi chilango chopweteka kwambiri : Nkhalamba ya chiwerewere, Mfumu ya bodza komanso Munthu osauka odzikweza.

Reference: صحيح مسلم، كتاب الإيمان، باب بيان غلظ تحريم...إلخ، الحدیث 107

Available in Other Languages