Hadith #152
Chichewa (Chicheŵa)Machimo akulu ndi awa: Kumphatikiza Allah ndi chinthu china, kusamvera makolo, kupha munthu (popanda chifukwa) komanso kulumbila zabodza.
Reference: صحيح البخاري، كتاب الأيمان والنذور، باب اليمين الغموس، الحدیث 6675

Machimo akulu ndi awa: Kumphatikiza Allah ndi chinthu china, kusamvera makolo, kupha munthu (popanda chifukwa) komanso kulumbila zabodza.
Reference: صحيح البخاري، كتاب الأيمان والنذور، باب اليمين الغموس، الحدیث 6675