
Hadith #250
Chichewa (Chicheŵa)Likanakhala kuti dziko lapansi ndilopambana kwa Allah ngakhale kufanana ndi phiko la udzudzu, sakanapereka ngakhale dontho limodzi lamadzi kwa munthu wosakhulupilira kuti amwe m'menemo.
Reference: جامع الترمذي، أبواب الزهد، باب ما جاء في هوان الدنيا على الله، الحدیث 2320