Hadith #249Hadith #249

Hadith #249

Chichewa (Chicheŵa)

Kulungama ndikukhala wamakhalidwe abwino, ndipo tchimo ndichomwe chimakusowetsa mtendere mumtima komanso sufuna kuti anthu achidziwe.

Reference: صحيح مسلم، كتاب البر والصلة والآداب، باب تفسير البر والإثم، الحدیث 2553

Available in Other Languages