
Hadith #313
Chichewa (Chicheŵa)Kodi sukudziwa kuti kulowa chisilamu kumafuta machimo akale onse, komanso msamuko umafufuta machimo onse akale monga momwenso mapemphero a Hajji yolandiridwa amafufutira machimo onse akale.
Reference: صحيح مسلم، كتاب الإيمان، باب كون الإسلام يهدم ما قبله وكذا الهجرة والحج، الحدیث 121