
Hadith #398
Chichewa (Chicheŵa)Kapolo wa Mulungu sadzasiya kuyankhidwa Dua yake ngati sakupempha za uchimo, kudula ubale komanso ngati sanena kuti ndapempha nthawi yaitali koma sindikuyankhidwa.
Reference: صحيح مسلم، كتاب الذكر والدعاء، باب بيان أنه يستجاب للداعي...إلخ، الحدیث 2735