
Hadith #209
Chichewa (Chicheŵa)Eeh iwe mwana wa Khattab! Ndikulumbilira kwa yemwe Mzimu wanga uli m'manja mwake, sanakupezepo satana ukuyenda njira, kupatula kuti amaisintha natenga njira ina posakhala yomwe umayenda iweyoyo (kuli kukuthawa).
Reference: صحيح البخاري، كتاب أصحاب النبي ﷺ، باب مناقب عمر بن الخطاب، الحدیث 3683