
Hadith #332
Chichewa (Chicheŵa)E inu anthu! Amene akudziwa kanthu kalikonse, ayenera kufotokoza, koma ngati sakudziwa, ayenera kunena kuti, Allah ndi amene akudziwa, pakuti ndichizindikiro chakudziwa, ndikulankhula kuti, Allah ndi amene akudziwa bwino kwa munthu sakudziwa.
Reference: صحیح البخاري، کتاب التفسیر، باب قوله: وما أنا من المتكلفين، الحدیث 4809