Hadith #238Hadith #238

Hadith #238

Chichewa (Chicheŵa)

Dziko lapansi sikanthu poyerekeza ndi dziko lili nkudza koma ngati chitsanzo cha m'modzi wa inu amene waviika chala chake m'nyanja nachivuulamo, ndiye awone madzi osalira kuchalacho. (Amenewo ndiwo dziko lapansi).

Reference: جامع الترمذي، أبواب الزهد، ‌‌باب ما جاء في هوان الدنيا على الله، الحدیث 2323

Available in Other Languages