Hadith #349Hadith #349

Hadith #349

Chichewa (Chicheŵa)

Dziko lapansi ndi lotembeleledwa ndipo chilichonse chili nkati mwakemonso nchotembeleledwa kupatula kumukumbukira Mulungu (dhikri) ndizomwe zimamuwandikisa munthu kwa Mulungu, Munthu ophunzira komanso ndiyemwe akusakasaka ma phunziro adini.

Reference: سنن ابن ماجه، كتاب الزهد، باب مثل الدنيا، الحدیث 4112

Available in Other Languages