
Hadith #273
Chichewa (Chicheŵa)Chulukitsani kumugwadira Allah, chifukwa ndithu simungamugwadire Allah kamodzi kupatula kuti Allah amakukwezani kudzera mu sajidayo mu ulemelero, komanso amakufufutirani tchimo limodzi.
Reference: صحيح مسلم، كتاب الصلاة، باب فضل السجود والحث عليه، الحدیث 488