Hadith #348Hadith #348

Hadith #348

Chichewa (Chicheŵa)

Chikhala kuti mwana wa Adam ali ndi chigwa cha Golide akanakondabe atakhala ndi zigwa ziwiri, ndipo palibe chingadzadzitse kamwa yake kupatula dothi ndipo Mulungu amalandira kulapa kwa yemwe walapa.

Reference: صحيح البخاري، كتاب الرقاق، ‌باب ما يتقى من فتنة المال...إلخ، الحدیث 6439

Available in Other Languages