
Hadith #377
Chichewa (Chicheŵa)Chikhala kuti mumayezamira mwa Allah kuyezamira kwenikweni akanakudyetsani ngati m'mene amadyesera mbalame, zimadzuka kummawa za njala koma zimabwera zitakhuta.
Reference: جامع الترمذي، أبواب الزهد، باب في التوكل على الله، الحدیث 2344