
Hadith #329
Chichewa (Chicheŵa)Chakudya cha munthu m'modzi ndichokwanira kudya anthu awiri, ndipo chakudya cha anthu awiri ndichokwanira anthu anayi chimodzimodzi nso chakudya cha anayi ndichokwanira kudya anthu asanu ndi atatu.
Reference: صحيح مسلم، كتاب الأشربة، باب فضيلة المواساة في الطعام القليل، الحدیث 2059