
Hadith #97
Chichewa (Chicheŵa)Anthu olungama akupita (akumwalira) m'modzi m'modzi mpakana adzatsala (anthu okhala ngati) madeya monga madeya a tirigu kapena tende. Allah sadzawalabadira mpang'ono pomwe.
Reference: صحيح البخاري، باب ذهاب الصالحين، كتاب الرقاق، الحدیث 6434