
Hadith #381
Chichewa (Chicheŵa)Allah amuchitire chifundo munthu amene ali odekha pa malonda ake, akagula, akagulitsa komanso pamene akudikilira kuti chilungamo chake chikwanilisidwe.
Reference: صحيح البخاري، كتاب البيوع، باب السهولة والسماحة...إلخ، الحدیث 2076